Salimo 62:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mukhulupirireni nthawi zonse, anthu inu.+Mukhuthulireni za mumtima mwanu.+Mulungu ndiye pothawirapo pathu.+ [Seʹlah.] Yesaya 26:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anthu inu muzidalira Yehova+ nthawi zonse, pakuti Ya* Yehova ndiye Thanthwe+ mpaka kalekale. Yeremiya 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Wodala ndi munthu aliyense amene amakhulupirira Yehova, amene amadalira Yehova.+
8 Mukhulupirireni nthawi zonse, anthu inu.+Mukhuthulireni za mumtima mwanu.+Mulungu ndiye pothawirapo pathu.+ [Seʹlah.]