Miyambo 28:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Munthu wodalira mtima wake ndi wopusa,+ koma woyenda mwanzeru ndi amene adzapulumuke.+ Yeremiya 9:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yehova wanena kuti: “Munthu wanzeru asadzitamande chifukwa cha nzeru zake.+ Munthu wamphamvu asadzitamande chifukwa cha mphamvu zake.+ Munthu wachuma asadzitamande chifukwa cha chuma chake.”+ Yeremiya 10:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ine ndikudziwa bwino, inu Yehova, kuti munthu wochokera kufumbi alibe ulamuliro wowongolera njira ya moyo wake. Munthu amene akuyenda alibe ulamuliro wowongolera mapazi ake.+ 1 Akorinto 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Munthu asamadzinyenge yekha: Ngati aliyense wa inu akudziyesa wanzeru+ mu nthawi* ino, akhale wopusa kuti akhale wanzeru.+
23 Yehova wanena kuti: “Munthu wanzeru asadzitamande chifukwa cha nzeru zake.+ Munthu wamphamvu asadzitamande chifukwa cha mphamvu zake.+ Munthu wachuma asadzitamande chifukwa cha chuma chake.”+
23 Ine ndikudziwa bwino, inu Yehova, kuti munthu wochokera kufumbi alibe ulamuliro wowongolera njira ya moyo wake. Munthu amene akuyenda alibe ulamuliro wowongolera mapazi ake.+
18 Munthu asamadzinyenge yekha: Ngati aliyense wa inu akudziyesa wanzeru+ mu nthawi* ino, akhale wopusa kuti akhale wanzeru.+