Hoseya 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Dama, vinyo wakale ndi vinyo wotsekemera zimawononga nzeru za munthu.+ Hoseya 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pa tsiku la chikondwerero cha mfumu yathu, akalonga adzidwalitsa+ ndipo ali ndi ukali chifukwa cha vinyo.+ Mfumuyo yatambasula dzanja lake pamodzi ndi anthu onyoza.
5 Pa tsiku la chikondwerero cha mfumu yathu, akalonga adzidwalitsa+ ndipo ali ndi ukali chifukwa cha vinyo.+ Mfumuyo yatambasula dzanja lake pamodzi ndi anthu onyoza.