Salimo 103:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tamanda amene akukukhululukira zolakwa zako zonse,+Iye amene akukuchiritsa matenda ako onse.+