Miyambo 27:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kudzudzula munthu mosabisa mawu, kuli bwino+ kusiyana ndi kumukonda koma osamusonyeza chikondicho. Miyambo 27:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zilonda zovulazidwa ndi munthu wokukonda zimakhala zokhulupirika,+ koma kuti munthu wodana nawe akupsompsone pamafunika kumuchonderera.+
6 Zilonda zovulazidwa ndi munthu wokukonda zimakhala zokhulupirika,+ koma kuti munthu wodana nawe akupsompsone pamafunika kumuchonderera.+