1 Mafumu 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nyumbayo anaimanga ndi miyala yosema+ kale, ndipo kulira kwa nyundo, nkhwangwa, kapena zida zilizonse zachitsulo sikunamveke m’nyumbayo+ pamene anali kuimanga. Luka 14:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mwachitsanzo, ndani wa inu amene akafuna kumanga nsanja sayamba wakhala pansi ndi kuwerengera ndalama zimene adzawononge,+ kuti aone ngati ali ndi ndalama zokwanira kumalizira nsanjayo?
7 Nyumbayo anaimanga ndi miyala yosema+ kale, ndipo kulira kwa nyundo, nkhwangwa, kapena zida zilizonse zachitsulo sikunamveke m’nyumbayo+ pamene anali kuimanga.
28 Mwachitsanzo, ndani wa inu amene akafuna kumanga nsanja sayamba wakhala pansi ndi kuwerengera ndalama zimene adzawononge,+ kuti aone ngati ali ndi ndalama zokwanira kumalizira nsanjayo?