Miyambo 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pita kwa nyerere+ waulesi iwe,+ ukaone mmene imachitira zinthu kuti ukhale wanzeru. Miyambo 22:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Waulesi amati:+ “Panja pali mkango!+ Ndithu undipha pakati pa bwalo la mzinda!”