Salimo 107:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Amenewa ndi amene aona ntchito za Yehova,+Ndiponso ntchito zake zodabwitsa m’madzi akuya.+