Luka 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma ukaitanidwa, pita ndipo ukakhale kumapeto kwenikweni,+ kuti munthu amene wakuitana uja akafika adzakuuze kuti, ‘Bwanawe, khala pamalo aulemuwa.’ Pamenepo udzalemekezeka pamaso pa alendo anzako onse.+
10 Koma ukaitanidwa, pita ndipo ukakhale kumapeto kwenikweni,+ kuti munthu amene wakuitana uja akafika adzakuuze kuti, ‘Bwanawe, khala pamalo aulemuwa.’ Pamenepo udzalemekezeka pamaso pa alendo anzako onse.+