Miyambo 11:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Amene amayendayenda n’kumanenera ena zoipa+ amaulula zinsinsi za anzake,+ koma wokhulupirika* amabisa nkhani.+ Miyambo 20:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Woyenda uku ndi uku n’kumanena zoipa za anthu ena amaulula zinsinsi,+ ndipo usamagwirizane ndi munthu wotengeka ndi milomo yake.+
13 Amene amayendayenda n’kumanenera ena zoipa+ amaulula zinsinsi za anzake,+ koma wokhulupirika* amabisa nkhani.+
19 Woyenda uku ndi uku n’kumanena zoipa za anthu ena amaulula zinsinsi,+ ndipo usamagwirizane ndi munthu wotengeka ndi milomo yake.+