Miyambo 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mthenga woipa amayambitsa mavuto,+ koma nthumwi yokhulupirika imachiritsa.+ Afilipi 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Komabe, ndaona kuti n’kofunika kutumiza Epafurodito kwa inu.+ Ameneyu ndi m’bale wanga, wantchito mnzanga+ ndi msilikali mnzanga.+ Komanso iye ndi nthumwi yanu ndi wonditumikira pa zosowa zanga.
25 Komabe, ndaona kuti n’kofunika kutumiza Epafurodito kwa inu.+ Ameneyu ndi m’bale wanga, wantchito mnzanga+ ndi msilikali mnzanga.+ Komanso iye ndi nthumwi yanu ndi wonditumikira pa zosowa zanga.