Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 22:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Pamenepo mfumu inauza asilikali othamanga+ amene anaima pamaso pake kuti: “Tembenukani ndi kupha ansembe a Yehova chifukwa ali kumbali ya Davide. Iwo anali kudziwanso kuti Davide ndi wothawa koma sanaulule kwa ine!”+ Koma atumiki a mfumuwo sanafune kutambasula manja awo kuti akanthe ansembe a Yehova.+

  • 2 Mbiri 24:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Mfumu Yehoasi sanakumbukire kukoma mtima kosatha kumene Yehoyada bambo a Zekariya anamusonyeza,+ ndipo anapha mwana wawo yemwe pakufa ananena kuti: “Yehova aone zimene mwachitazi ndi kubwezera.”+

  • Machitidwe 7:52
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 52 Ndi mneneri uti amene makolo anuwo sanamuzunze?+ Inde, iwo anapha+ amene analengezeratu za kubwera kwa Wolungamayo,+ amene inuyo munamupereka ndi kumupha,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena