Miyambo 27:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mlendo akutamande, osati pakamwa pako. Munthu wochokera kudziko lina achite zimenezo, osati milomo yako.+ Yohane 5:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Mungakhulupirire bwanji, pamene mumalandira ulemerero+ kuchokera kwa anthu anzanu, koma osayesetsa kupeza ulemerero wochokera kwa Mulungu yekhayo?+ Afilipi 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Musachite chilichonse ndi mtima wokonda mikangano+ kapena wodzikuza,+ koma modzichepetsa, ndi kuona ena kukhala okuposani.+
2 Mlendo akutamande, osati pakamwa pako. Munthu wochokera kudziko lina achite zimenezo, osati milomo yako.+
44 Mungakhulupirire bwanji, pamene mumalandira ulemerero+ kuchokera kwa anthu anzanu, koma osayesetsa kupeza ulemerero wochokera kwa Mulungu yekhayo?+
3 Musachite chilichonse ndi mtima wokonda mikangano+ kapena wodzikuza,+ koma modzichepetsa, ndi kuona ena kukhala okuposani.+