-
Yohane 9:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Iye anawayankha kuti: “Ndakuuzani kale, koma inu simunamvetsere. Nanga n’chifukwa chiyani mukufuna kumvanso? Kapena inunso mukufuna kukhala ophunzira ake?”
-