Miyambo 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi ugonabe mpaka liti, waulesiwe?+ Udzuka nthawi yanji kutulo tako?+ Miyambo 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ulesi umachititsa tulo tofa nato,+ ndipo munthu waulesi amakhala ndi njala.+ Miyambo 24:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ukati, “Ndigoneko pang’ono, ndibeko katulo pang’ono, ndipindeko manja pang’ono pogona,”+