Miyambo 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Njira ya munthu wopusa imakhala yolondola m’maso mwake,+ koma womvera malangizo ndi wanzeru.+