Luka 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iye anamuuza kuti: “Munthu iwe, ndani anandiika ine kukhala woweruza+ kapena wogawa chuma chanu?” 1 Atesalonika 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiponso muyesetse kukhala mwamtendere,+ kusalowerera mu nkhani za eni,+ ndi kugwira ntchito ndi manja anu+ monga mmene tinakulamulirani. 1 Petulo 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma pasakhale wina wa inu wovutika+ chifukwa cha kupha munthu, kuba, kuchita choipa china kapena kulowerera nkhani za ena.+
11 Ndiponso muyesetse kukhala mwamtendere,+ kusalowerera mu nkhani za eni,+ ndi kugwira ntchito ndi manja anu+ monga mmene tinakulamulirani.
15 Koma pasakhale wina wa inu wovutika+ chifukwa cha kupha munthu, kuba, kuchita choipa china kapena kulowerera nkhani za ena.+