Aefeso 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koposa zonse, nyamulani chishango chachikulu chachikhulupiriro,+ chimene mudzathe kuzimitsira mivi yonse yoyaka moto+ ya woipayo.
16 Koposa zonse, nyamulani chishango chachikulu chachikhulupiriro,+ chimene mudzathe kuzimitsira mivi yonse yoyaka moto+ ya woipayo.