Miyambo 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pali zinthu 6 zimene Yehova amadana nazo.+ Zilipo zinthu 7 zimene moyo wake umanyansidwa nazo:+