Genesis 37:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kenako, iwo anatumiza mkanjo wamizeremizere uja kwa bambo awo. Atafika nawo anati: “Tapeza mkanjo uwu. Chonde, uonetsetseni+ kuti muone ngati uli mkanjo wa mwana wanu kapena ayi.”+
32 Kenako, iwo anatumiza mkanjo wamizeremizere uja kwa bambo awo. Atafika nawo anati: “Tapeza mkanjo uwu. Chonde, uonetsetseni+ kuti muone ngati uli mkanjo wa mwana wanu kapena ayi.”+