Salimo 25:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ubwenzi wolimba ndi Yehova ndi wa anthu amene amamuopa,+Pangano lakenso ndi la anthu oterowo, ndipo iye amawadziwitsa panganolo.+ Maliko 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndipo iye anayamba kuwauza kuti: “Inu mwapatsidwa mwayi wozindikira chinsinsi chopatulika+ cha ufumu wa Mulungu. Koma kwa amene ali kunja zonse zimachitika mwa mafanizo,+ Yakobo 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho ngati wina akusowa nzeru,+ azipempha kwa Mulungu,+ ndipo adzamupatsa,+ popeza iye amapereka mowolowa manja kwa onse ndiponso amapereka mosatonza.+
14 Ubwenzi wolimba ndi Yehova ndi wa anthu amene amamuopa,+Pangano lakenso ndi la anthu oterowo, ndipo iye amawadziwitsa panganolo.+
11 Ndipo iye anayamba kuwauza kuti: “Inu mwapatsidwa mwayi wozindikira chinsinsi chopatulika+ cha ufumu wa Mulungu. Koma kwa amene ali kunja zonse zimachitika mwa mafanizo,+
5 Choncho ngati wina akusowa nzeru,+ azipempha kwa Mulungu,+ ndipo adzamupatsa,+ popeza iye amapereka mowolowa manja kwa onse ndiponso amapereka mosatonza.+