1 Mafumu 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Choka kuno, lowera chakum’mawa ukabisale+ m’chigwa* cha Keriti, chimene chili kum’mawa kwa Yorodano. Miyambo 29:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Olungama akachuluka, anthu amasangalala,+ koma aliyense woipa akayamba kulamulira, anthu amabuula.+
3 “Choka kuno, lowera chakum’mawa ukabisale+ m’chigwa* cha Keriti, chimene chili kum’mawa kwa Yorodano.
2 Olungama akachuluka, anthu amasangalala,+ koma aliyense woipa akayamba kulamulira, anthu amabuula.+