Levitiko 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “‘Musamaweruze mopanda chilungamo. Musamakondere munthu wosauka,+ ndiponso musamakondere munthu wolemera.+ Mnzako uzimuweruza mwachilungamo. Deuteronomo 16:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Usamapotoze chiweruzo.+ Usamakondere+ kapena kulandira chiphuphu, chifukwa chiphuphu chimachititsa khungu maso a anthu anzeru+ ndi kupotoza mawu a anthu olungama. Miyambo 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kukondera munthu woipa si bwino.+ Komanso si bwino kukankhira pambali munthu wolungama poweruza.+ Yakobo 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Abale anga, kodi mukuganiza kuti mukukhulupirira Ambuye wathu Yesu Khristu, amene ali ulemerero+ wathu, pamene mukuchita zokondera?+
15 “‘Musamaweruze mopanda chilungamo. Musamakondere munthu wosauka,+ ndiponso musamakondere munthu wolemera.+ Mnzako uzimuweruza mwachilungamo.
19 Usamapotoze chiweruzo.+ Usamakondere+ kapena kulandira chiphuphu, chifukwa chiphuphu chimachititsa khungu maso a anthu anzeru+ ndi kupotoza mawu a anthu olungama.
2 Abale anga, kodi mukuganiza kuti mukukhulupirira Ambuye wathu Yesu Khristu, amene ali ulemerero+ wathu, pamene mukuchita zokondera?+