1 Mafumu 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndikupatsanso zomwe sunapemphe,+ chuma+ ndi ulemerero, moti sikudzakhalanso mfumu ngati iwe masiku ako onse.+ Salimo 84:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inu Yehova wa makamu, wodala ndi munthu amene amakhulupirira inu.+
13 Ndikupatsanso zomwe sunapemphe,+ chuma+ ndi ulemerero, moti sikudzakhalanso mfumu ngati iwe masiku ako onse.+