Salimo 97:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kuwala kwaunikira wolungama,+Ndipo anthu owongoka mtima akusangalala.+ 1 Petulo 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ngakhale kuti simunamuonepo, mumamukonda.+ Ngakhale simukumuona panopa, mumakhulupirira mwa iye ndipo mukusangalala kwambiri ndi chimwemwe chachikulu ndiponso chosaneneka,
8 Ngakhale kuti simunamuonepo, mumamukonda.+ Ngakhale simukumuona panopa, mumakhulupirira mwa iye ndipo mukusangalala kwambiri ndi chimwemwe chachikulu ndiponso chosaneneka,