Yeremiya 38:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiyeno Ebedi-meleki Mwitiyopiya anauza Yeremiya kuti: “Kulunga zingwezo ndi nsanza komanso ndi zidutswa za nsalu ndipo uziike m’khwapa.” Yeremiya anachitadi zomwezo.+ Maliko 10:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Pakuti ngakhale Mwana wa munthu sanabwere kudzatumikiridwa,+ koma kudzatumikira ndi kudzapereka moyo wake dipo+ kuwombola anthu ambiri.”+
12 Ndiyeno Ebedi-meleki Mwitiyopiya anauza Yeremiya kuti: “Kulunga zingwezo ndi nsanza komanso ndi zidutswa za nsalu ndipo uziike m’khwapa.” Yeremiya anachitadi zomwezo.+
45 Pakuti ngakhale Mwana wa munthu sanabwere kudzatumikiridwa,+ koma kudzatumikira ndi kudzapereka moyo wake dipo+ kuwombola anthu ambiri.”+