Miyambo 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti Yehova amapereka nzeru.+ Kudziwa zinthu ndi kuzindikira kumatuluka m’kamwa mwake.+ Miyambo 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nzerutu ikungokhalira kufuula,+ ndipo kuzindikira kukungokhalira kutulutsa mawu.+