Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 27:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Chinthu chimodzi chimene ndapempha kwa Yehova,+

      Chimenecho ndi chimene ndimachikhumba,+

      N’chakuti, ndikhale m’nyumba ya Yehova masiku onse a moyo wanga,+

      Kuti ndione ubwino wa Yehova,+

      Komanso kuti ndiyang’ane kachisi wake moyamikira.+

  • Luka 10:42
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Komatu zinthu zofunika kwenikweni n’zochepa+ chabe, mwinanso n’chimodzi chokha basi. Kumbali yake, Mariya wasankha chinthu chabwino kwambiri,+ ndipo sadzalandidwa chinthu chimenechi.”

  • 1 Yohane 3:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 ndipo chilichonse chimene tingapemphe, iye adzatipatsa,+ chifukwa tikusunga malamulo ake ndi kuchita zinthu zomukondweretsa.+

  • 1 Yohane 5:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ifetu timamudalira+ kuti chilichonse chimene tingamupemphe mogwirizana ndi chifuniro chake, amatimvera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena