Yobu 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma funsa nyama zoweta ndipo zikulangiza.+Komanso zouluka zam’mlengalenga, ndipo zikuuza.+ Yobu 35:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iye ndiye amatiphunzitsa+ zambiri kuposa nyama zakutchire,+Ndipo amatipatsa nzeru kuposa ngakhale zolengedwa zouluka m’mlengalenga.
11 Iye ndiye amatiphunzitsa+ zambiri kuposa nyama zakutchire,+Ndipo amatipatsa nzeru kuposa ngakhale zolengedwa zouluka m’mlengalenga.