Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 91:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Iwo adzakunyamula m’manja mwawo,+

      Kuti phazi lako lisawombe mwala uliwonse.+

  • Salimo 121:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Iye sangalole kuti phazi lako lipunthwe.+

      Amene amakuyang’anira sangawodzere.+

  • Miyambo 4:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ukamayenda, sudzayenda mopanikizika+ ndipo ngati ukuthamanga sudzapunthwa.+

  • Yesaya 26:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Njira ya munthu wolungama ndi yowongoka.+ Popeza inu ndinu wochita zowongoka, mudzasalaza njira ya munthu wolungama.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena