Salimo 104:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 M’mapiri aatali+ ndi mmene mumakhala mbuzi zakumapiri.+Ndipo m’mapanga ndiye mothawiramo mbira.+