Ekisodo 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndipo dzombelo linayamba kufika m’dziko lonse la Iguputo ndi kutera m’madera onse a dzikolo.+ Linawasautsa kwambiri.+ Dzombe ngati limeneli linali lisanagwepo n’kale lonse ndipo sipadzagwanso lina ngati limeneli. Salimo 105:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Analamula kuti pagwe dzombe,+Ndipo panagwa dzombe losawerengeka la mtundu winawake.+ Yoweli 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zinthu zimene mbozi zinasiya zinadyedwa ndi dzombe.+ Zimene dzombelo linasiya zinadyedwa ndi ana a dzombe oyenda pansi opanda mapiko ndipo zimene ana a dzombe oyenda pansiwo anasiya zinadyedwa ndi mphemvu.+
14 Ndipo dzombelo linayamba kufika m’dziko lonse la Iguputo ndi kutera m’madera onse a dzikolo.+ Linawasautsa kwambiri.+ Dzombe ngati limeneli linali lisanagwepo n’kale lonse ndipo sipadzagwanso lina ngati limeneli.
4 Zinthu zimene mbozi zinasiya zinadyedwa ndi dzombe.+ Zimene dzombelo linasiya zinadyedwa ndi ana a dzombe oyenda pansi opanda mapiko ndipo zimene ana a dzombe oyenda pansiwo anasiya zinadyedwa ndi mphemvu.+