Yobu 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tembenuzirani nkhope zanu kwa ine n’kundiyang’ana modabwa,Ndipo muike dzanja lanu pakamwa.+ Miyambo 27:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mlendo akutamande, osati pakamwa pako. Munthu wochokera kudziko lina achite zimenezo, osati milomo yako.+
2 Mlendo akutamande, osati pakamwa pako. Munthu wochokera kudziko lina achite zimenezo, osati milomo yako.+