Salimo 71:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kuyambira ndili m’mimba mwa mayi anga inu mwandithandiza.+Inu ndi amene munanditulutsa m’mimba mwa mayi anga.+Ndimatamanda inu nthawi zonse.+ Yesaya 49:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kodi mayi angaiwale mwana wake woyamwa, osamvera chisoni mwana wochokera m’mimba mwake?+ Ngakhale amayi amenewa akhoza kuiwala,+ koma ine sindidzakuiwala.+
6 Kuyambira ndili m’mimba mwa mayi anga inu mwandithandiza.+Inu ndi amene munanditulutsa m’mimba mwa mayi anga.+Ndimatamanda inu nthawi zonse.+
15 Kodi mayi angaiwale mwana wake woyamwa, osamvera chisoni mwana wochokera m’mimba mwake?+ Ngakhale amayi amenewa akhoza kuiwala,+ koma ine sindidzakuiwala.+