1 Samueli 25:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Iwenso udalitsike chifukwa cha kulingalira bwino kwako.+ Udalitsike chifukwa cha kundigwira lero kuti ndisapalamule mlandu wamagazi+ ndi kudzipulumutsa ndekha ndi dzanja langa.+ Miyambo 24:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iweyo udzatha kumenya nkhondo yako potsatira malangizo anzeru,+ ndipo pakakhala aphungu ochuluka anthu amapulumuka.+
33 Iwenso udalitsike chifukwa cha kulingalira bwino kwako.+ Udalitsike chifukwa cha kundigwira lero kuti ndisapalamule mlandu wamagazi+ ndi kudzipulumutsa ndekha ndi dzanja langa.+
6 Iweyo udzatha kumenya nkhondo yako potsatira malangizo anzeru,+ ndipo pakakhala aphungu ochuluka anthu amapulumuka.+