Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 19:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Chotero Yonatani analankhula zabwino+ za Davide kwa Sauli bambo ake, kuti: “Mfumu isachimwire+ mtumiki wake Davide, chifukwa iye sanakuchimwireni, ndipo wakhala akukuchitirani zinthu zabwino kwambiri.+

  • 1 Samueli 22:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ahimeleki anayankha mfumuyo kuti: “Ndani pakati pa atumiki anu onse ali ngati Davide,+ munthu wokhulupirika,+ mkamwini+ wa mfumu, mtsogoleri wa asilikali okulonderani ndiponso munthu wolemekezeka m’nyumba yanu?+

  • Esitere 4:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Pakuti ngati iwe ukhala chete pa nthawi ino, thandizo ndi chipulumutso cha Ayuda zidzachokera kwina.+ Koma anthu inu, iwe ndi nyumba ya bambo ako, nonse mudzatheratu. Ndipo ndani akudziwa? Mwina iwe wakhala mfumukazi kuti uthandize pa nthawi ngati imeneyi.”+

  • Esitere 7:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pamenepo Mfumukazi Esitere inayankha kuti: “Ngati mungandikomere mtima mfumu, ndipo ngati zingakukomereni, ndikupempha kuti mupulumutse moyo wanga+ komanso kuti musawononge anthu a mtundu wanga.+

  • Salimo 82:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Pulumutsani munthu wonyozeka ndi wosauka.+

      Alanditseni m’manja mwa anthu oipa.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena