1 Samueli 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Komanso chaka ndi chaka mayi ake anali kumusokera kamalaya kakunja kodula manja. Iwo anali kumubweretsera kamalayako akabwera ndi mwamuna wawo kudzapereka nsembe ya pachaka.+ Machitidwe 9:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Pamenepo Petulo ananyamuka n’kupita nawo limodzi. Atafika kumeneko, iwo anamutengera m’chipinda cham’mwamba chija. Ndipo akazi onse amasiye anabwera kwa iye akulira ndi kumuonetsa malaya ambiri akunja ndi amkati+ amene Dorika anali kusoka pamene anali nawo.+ Tito 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 kukhala oganiza bwino, oyera,+ ogwira ntchito zapakhomo, abwino ndi ogonjera+ amuna awo, kuti mawu a Mulungu asanyozedwe.+
19 Komanso chaka ndi chaka mayi ake anali kumusokera kamalaya kakunja kodula manja. Iwo anali kumubweretsera kamalayako akabwera ndi mwamuna wawo kudzapereka nsembe ya pachaka.+
39 Pamenepo Petulo ananyamuka n’kupita nawo limodzi. Atafika kumeneko, iwo anamutengera m’chipinda cham’mwamba chija. Ndipo akazi onse amasiye anabwera kwa iye akulira ndi kumuonetsa malaya ambiri akunja ndi amkati+ amene Dorika anali kusoka pamene anali nawo.+
5 kukhala oganiza bwino, oyera,+ ogwira ntchito zapakhomo, abwino ndi ogonjera+ amuna awo, kuti mawu a Mulungu asanyozedwe.+