Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 27:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Yehova ndiye kuwala+ kwanga ndi chipulumutso changa.+

      Ndingaopenso ndani?+

      Yehova ndiye malo a chitetezo cha moyo wanga.+

      Ndingachitenso mantha ndi ndani?+

  • Danieli 3:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ngati mungatiponyere m’ng’anjo yoyaka moto, Mulungu wathu amene tikumutumikira akhoza kutipulumutsa. Iye atipulumutsa m’ng’anjo yoyaka moto ndiponso m’manja mwanu mfumu.+

  • Luka 1:74
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 74 kuti pambuyo pakuti tapulumutsidwa m’manja mwa adani,+ atipatse mwayi wochita utumiki wopatulika kwa iye+ mopanda mantha,

  • Yohane 14:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “Mitima yanu isavutike.+ Khulupirirani Mulungu,+ khulupiriraninso ine.+

  • Afilipi 1:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Abale ambiri mwa Ambuye, alimba mtima chifukwa cha kumangidwa kwanga, ndipo akuonetsa kulimba mtima kowonjezereka polankhula mawu a Mulungu mopanda mantha.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena