1 Timoteyo 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 wodziwika kuti anachita ntchito zabwino,+ analera bwino ana,+ anali kuchereza alendo,+ anasambitsa mapazi a oyera,+ anathandiza ena m’masautso,+ ndiponso anali kugwira mwakhama ntchito iliyonse yabwino.+
10 wodziwika kuti anachita ntchito zabwino,+ analera bwino ana,+ anali kuchereza alendo,+ anasambitsa mapazi a oyera,+ anathandiza ena m’masautso,+ ndiponso anali kugwira mwakhama ntchito iliyonse yabwino.+