Genesis 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pambuyo pake Mulungu anafikira Abimeleki usiku m’maloto n’kumuuza kuti: “Ufatu iwe chifukwa cha mkazi amene watengayu,+ pakuti ndi mkazi wa mwini.”+ Deuteronomo 22:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Mwamuna akapezeka akugona ndi mkazi wa mwiniwake,+ mwamuna ndi mkaziyo, onsewo azifera pamodzi. Mwamuna wogona ndi mkaziyo ndiponso mkaziyo azifera pamodzi.+ Motero uzichotsa oipawo mu Isiraeli.+ 2 Samueli 11:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pamenepo mkazi wa Uriya anamva kuti Uriya mwamuna wake+ wafa, ndipo anayamba kumulira.+ 1 Akorinto 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 ndiponso mwamuna sanalengedwere mkazi, koma mkazi analengedwera mwamuna.+
3 Pambuyo pake Mulungu anafikira Abimeleki usiku m’maloto n’kumuuza kuti: “Ufatu iwe chifukwa cha mkazi amene watengayu,+ pakuti ndi mkazi wa mwini.”+
22 “Mwamuna akapezeka akugona ndi mkazi wa mwiniwake,+ mwamuna ndi mkaziyo, onsewo azifera pamodzi. Mwamuna wogona ndi mkaziyo ndiponso mkaziyo azifera pamodzi.+ Motero uzichotsa oipawo mu Isiraeli.+