Genesis 24:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Choncho, iye mwamsanga anakhuthulira madzi amene anali mumtsuko aja muchomweramo ziweto. Kenako anayamba kuthamanga mobwerezabwereza kukatunga madzi ena pachitsimepo+ mpaka ngamila zonse za mlendoyo zitamwa mokwanira. Oweruza 5:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Yaeli,+ mkazi wa Hiberi Mkeni,+ akhale wodalitsika pakati pa akazi onse,Akhale wodalitsika pakati pa akazi onse okhala m’mahema.+ Yobu 40:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tadziveka ukulu+ ndiponso kukwezeka,+Ndipo uvale ulemu+ ndi ulemerero.+
20 Choncho, iye mwamsanga anakhuthulira madzi amene anali mumtsuko aja muchomweramo ziweto. Kenako anayamba kuthamanga mobwerezabwereza kukatunga madzi ena pachitsimepo+ mpaka ngamila zonse za mlendoyo zitamwa mokwanira.
24 Yaeli,+ mkazi wa Hiberi Mkeni,+ akhale wodalitsika pakati pa akazi onse,Akhale wodalitsika pakati pa akazi onse okhala m’mahema.+