Mateyu 6:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Musamade nkhawa za tsiku lotsatira,+ chifukwa tsiku lotsatira lidzakhala ndi zodetsa nkhawa zakenso. Zoipa za tsiku lililonse n’zokwanira pa tsikulo.
34 Musamade nkhawa za tsiku lotsatira,+ chifukwa tsiku lotsatira lidzakhala ndi zodetsa nkhawa zakenso. Zoipa za tsiku lililonse n’zokwanira pa tsikulo.