Genesis 30:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mwanayo atabadwa, Leya anati: “Ndasangalala kwambiri! Akazi adzanditcha wodala.”+ Chotero Leya anatcha mwanayo dzina lakuti Aseri.*+
13 Mwanayo atabadwa, Leya anati: “Ndasangalala kwambiri! Akazi adzanditcha wodala.”+ Chotero Leya anatcha mwanayo dzina lakuti Aseri.*+