Salimo 35:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iwo salankhula mawu amtendere,+Koma amakonzera chiwembu anthu ofatsa a padziko lapansi,Kuti awachitire zachinyengo.+ Salimo 55:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iye watambasula dzanja lake kuukira anthu amene ali naye pa mtendere.+Wanyoza pangano lake.+
20 Iwo salankhula mawu amtendere,+Koma amakonzera chiwembu anthu ofatsa a padziko lapansi,Kuti awachitire zachinyengo.+