Miyambo 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Njira yako ikhale kutali ndi iye. Usayandikire pakhomo la nyumba yake,+ 2 Akorinto 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Musamangidwe m’goli ndi osakhulupirira, chifukwa ndinu osiyana.+ Pali ubale wotani pakati pa chilungamo ndi kusamvera malamulo?+ Kapena pali kugwirizana kotani pakati pa kuwala ndi mdima?+ 1 Atesalonika 5:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pewani zoipa zamtundu uliwonse.+
14 Musamangidwe m’goli ndi osakhulupirira, chifukwa ndinu osiyana.+ Pali ubale wotani pakati pa chilungamo ndi kusamvera malamulo?+ Kapena pali kugwirizana kotani pakati pa kuwala ndi mdima?+