Miyambo 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zidzaika nkhata yamaluwa yokongola kumutu kwako.+ Zidzakuveka chisoti chachifumu chokongola.”+