Miyambo 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 ukamvetsera nzeru ndi khutu lako,+ ukaika mtima wako pa kuzindikira,+ Yakobo 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Abale anga okondedwa, dziwani izi: Munthu aliyense akhale wofulumira kumva, wodekha polankhula,+ wosafulumira kukwiya,+
19 Abale anga okondedwa, dziwani izi: Munthu aliyense akhale wofulumira kumva, wodekha polankhula,+ wosafulumira kukwiya,+