Miyambo 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Onse ogona naye sadzabwerera ndipo iwo sadzapezanso njira za amoyo.+ Miyambo 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma mwamunayo sakudziwa kuti kumeneko kuli akufa, ndiponso kuti amene amaitanidwa ndi mkaziyu ali kumalo otsika a ku Manda.+
18 Koma mwamunayo sakudziwa kuti kumeneko kuli akufa, ndiponso kuti amene amaitanidwa ndi mkaziyu ali kumalo otsika a ku Manda.+