Miyambo 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mwana wanga, ukamvera mawu anga+ ndi kusunga malamulo anga ngati chuma chamtengo wapatali,+