Miyambo 31:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Usamapereke mphamvu zako kwa akazi,+ ndipo usamapereke njira zako ku zinthu zimene zimachititsa mafumu kufafanizidwa.+ Luka 15:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Koma atangofika mwana wanuyu,+ amene anadya chuma chanu ndi mahule,+ mwamuphera mwana wa ng’ombe wamphongo wonenepa bwino.’+
3 Usamapereke mphamvu zako kwa akazi,+ ndipo usamapereke njira zako ku zinthu zimene zimachititsa mafumu kufafanizidwa.+
30 Koma atangofika mwana wanuyu,+ amene anadya chuma chanu ndi mahule,+ mwamuphera mwana wa ng’ombe wamphongo wonenepa bwino.’+